2 Samuel 23:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mzimu wa Chauta ukulankhula mwa ine, mau ake ali pakamwa panga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mzimu wa Yehova unalankhula mwa ine, ndi mau ake anali pa lilime langa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mzimu wa Yehova unayankhula kudzera mwa ine; mawu ake anali pakamwa panga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mzimu wa Yehova unalankhula mwa ine, Ndi mau ace anali pa lilime langa,