2 Samuel 23:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimenezi ndi ntchito zimene adatchuka nazo Benaya mwana wa Yehoyada, yemwe anali m'modzi wa anthu makumi atatu amphamvu aja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Izi anachita Benaya mwana wa Yehoyada, natenga dzina mwa ngwazi zitatuzo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Izi ndi zamphamvu zimene Benaya mwana wa Yehoyada anachita. Iyeyo analinso wotchuka ngati anthu atatu amphamvu aja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Izi anacita Benaya mwana wa Yehoyada, natenga dzina mwa ngwazi zitatuzo.