2 Samuel 23:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'gulu la anthu makumi atatu aja munalinso aŵa: Asahele, mbale wa Yowabu, Elihanani, mwana wa Dodo, wa ku Betelehemu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Asahele mbale wa Yowabu anali wa makumi atatuwo; Elihanani mwana wa Dodo wa ku Betelehemu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼgulu la anthu makumi atatu aja munalinso awa: Asaheli mʼbale wa Yowabu, Elihanani mwana wa Dodo wa ku Betelehemu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Asaheli mbale wa Yoabu anali wa makumi atatuwo; Elihanani mwana wa Dodo wa ku Betelehemu;