2 Samuel 23:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Panalinso Benaya wa ku Piratoni, Hidai wa ku mitsinje ya ku Gaasi,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Benaya Mpiratoni, Hidai wa ku timitsinje ta Gaasi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Benaya Mpiratoni, Hidayi wa ku zigwa za Gaasi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Benaya Mpiratoni, Hidai wa ku timitsinje ta Gaasi;