2 Samuel 23:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma anthu oipa onse amachotsedwa ngati minga. Anthu satha kuigwira ndi manja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma oipa onse adzakhala ngati minga yoyenera kuitaya, pakuti siigwiridwa ndi dzanja;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma anthu oyipa ndiwo ayenera kutayidwa kunja ngati minga, imene sitengedwa ndi manja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma oipa onse adzakhala ngati minga yoyenera kuitaya, Pakuti siigwiridwa ndi dzanja;