2 Samuel 23:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma amaidula ndi chigwandali nakaitentha pa moto.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma wakukhudza iyo adzikonzeratu chitsulo ndi luti la mkondo; ndipo idzatenthedwa konse ndi moto m'malo mwao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aliyense amene wayikhudza mingayo amayidula pogwiritsa ntchito chigwandali kapena ndodo ya mkondo; nayitentha pa moto.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma wakukhudza iyo adzikonzeratu citsulo ndi luti la mkondo; Ndipo idzatenthedwa konse ndi mota m'malo mwao.