2 Samuel 24:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atamva mau a Gadiwo, Davide adapita monga momwe Chauta adaalamulira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Davide anakwerako monga mwa kunena kwa Gadi, monga adalamulira Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Davide anapita monga momwe Yehova anamulamulira kudzera mwa Gadi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Davide anakwerako monga mwa kunena kwa Gadi, monga adalamulira Yehova.