2 Samuel 24:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adafika ku Giliyadi ndi ku Kadesi m'dziko la Ahiti, nakafika ku Dani, kuchokera kumeneko adayenda mozungulira ku Sidoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nafika ku Giliyadi ndi ku dera la Tatimuhodisi; nafika ku Dani-Yaana ndi kuzungulira, kufikira ku Sidoni,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anapita ku Giliyadi ndi ku chigwa cha Tahitimu Hodisi ndipo anapitirira mpaka ku Dani Yaani ndi madera ozungulira Sidoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nafika ku Gileadi ndi ku dera la Tatimuhodisi; nafika ku Dani-Jaana ndi kuzungulira, kufikira ku Zidoni,