2 Samuel 24:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero, atabzola dziko lonselo, adadzafika ku Yerusalemu itatha miyezi isanu ndi inai ndi masiku makumi aŵiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chomwecho pamene atayenda dziko lonse anafika ku Yerusalemu pakutha miyezi isanu ndi inai, ndi masiku makumi awiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atayendayenda mʼdziko lonse anabwerera ku Yerusalemu patapita miyezi isanu ndi inayi ndi masiku makumi awiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Comweco pamene atayenda dziko lonse anafika ku Yerusalemu pakutha miyezi isanu ndi inai, ndi masiku makumi awiri.