2 Samuel 3:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo Isiboseti adangoti kukamwa yasa, osatha kumuyankha Abinere mau ndi amodzi omwe, chifukwa ankamuwopa kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iye sanakhoze kuyankha Abinere mau amodzi chifukwa cha kumuopa iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Isiboseti sanayerekezenso kunena mawu ena kwa Abineri, chifukwa ankamuopa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iye sanakhoza kuyankha Abineri mau amodzi cifukwa ca kumuopa iye.