2 Samuel 3:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Davide adabereka ana aamuna ku Hebroni. Mwana wake woyamba anali Aminoni, wobadwa kwa Ahinowamu wa ku Yezireele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ana a Davide anabadwira ku Hebroni. Mwana woyamba ndiye Aminoni, wa Ahinowamu wa ku Yezireele;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana aamuna a Davide amene anabadwira ku Hebroni anali awa: Woyamba anali Amnoni, amayi ake anali Ahinoamu wa ku Yezireeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ana a Davide anabadwira ku Hebroni. Mwana woyamba ndiye Amnoni, wa Ahinoamu wa ku Jezreeli;