2 Samuel 3:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake Davide atamva, adati, “Ine pamodzi ndi anthu a mu ufumu wanga tilibe ndi mlandu womwe pamaso pa Chauta pa imfa ya Abinere, mwana wa Nere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pambuyo pake, pakuchimva Davide, anati, Ine ndi ufumu wanga tikhala osachimwira mwazi wa Abinere mwana wa Nere, nthawi zonse, pamaso pa Yehova;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Patapita nthawi, Davide atamva zimenezi anati, “Ine ndi ufumu wanga tidzakhala osalakwa pamaso pa Yehova pa imfa ya Abineri mwana wa Neri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pambuyo pace, pakucimva Davide, anati, Ine ndi ufumu wanga tikhala osacimwira mwazi wa Abineri mwana wa Neri, nthawi zonse, pamaso pa Yehova;