2 Samuel 3:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wachinai anali Adoniya, wobadwa kwa Hagiti. Wachisanu anali Sefatiya wobadwa kwa Abitala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi wachinai Adoniya mwana wa Hagiti; ndi wachisanu Sefatiya mwana wa Abitala;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
wachinayi anali Adoniya, amayi ake anali Hagiti; wachisanu, Sefatiya amayi ake anali Abitali;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi wacinai Adoniya mwana wa Hagiti; ndi wacisanu Sefatiya mwana wa Abitali;