2 Samuel 3:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene kunali nkhondo pakati pa anthu a Saulo ndi anthu a Davide, Abinere adayamba kudzipatsa mphamvu pa anthu a Saulo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo panali, pokhala nkhondo pakati pa nyumba ya Saulo ndi nyumba ya Davide, Abinere analimbikira nyumba ya Saulo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene kunali nkhondo pakati pa banja la Sauli ndi banja la Davide, Abineri anayamba kudzipatsa yekha mphamvu pakati pa banja la Sauli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo panali, pokhala nkhondo pakati pa nyumba ya Sauli ndi nyumba ya Davide, Abineri analimbikira nyumba ya Sauli.