2 Samuel 4:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Abeeroti adathaŵira ku Gitaimu, ndipo akhala akukhala nao kumeneko mpaka pano).
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi Abeeroti anathawira ku Gitaimu; kumeneko amakhalira kufikira lero lino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
chifukwa anthu a ku Beeroti anathawira ku Gitaimu ndipo akhala ali kumeneko ngati alendo mpaka lero lino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi Abeeroti anathawira ku Gitaimu; kumeneko amakhalira kufikira lero lino.