2 Samuel 5:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero mphamvu za Davide zidanka zikulirakulira, chifukwa Chauta, Mulungu Wamphamvuzonse, anali naye.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Davide anakula chikulire chifukwa Yehova Mulungu wa makamu anali naye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo mphamvu za Davide zinkakulirakulira chifukwa anali ndi Yehova Mulungu Wamphamvuzonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Davide anakula cikulire cifukwa Yehova Mulungu wa makamu anali naye.