2 Samuel 5:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Davide anali wa zaka makumi atatu za kubadwa pamene adaloŵa ufumu. Adakhala mu ufumu zaka makumi anai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Davide anali ndi zaka makumi atatu polowa iye ufumu wake, nakhala mfumu zaka makumi anai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide anali ndi zaka makumi atatu pamene anakhala mfumu, ndipo analamulira zaka makumi anayi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Davide anali ndi zaka makumi atatu polowa iye ufumu wace, nakhala mfumu zaka makumi anai.