2 Samuel 6:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Mikala, mwana wa Saulo, adaferamo osamuwona mwana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Mikala mwana wamkazi wa Saulo sanaone mwana kufikira tsiku la imfa yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Mikala mwana wa Sauli sanakhalenso ndi mwana mpaka anamwalira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Mikala mwana wamkazi wa Sauli sanaona mwana kufikira tsiku la imfa yace.