2 Samuel 7:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma sindidzamchotsera chikondi changa chosasinthika, monga m'mene ndidaachitira ndi Saulo, amene ndidamkana, kuti uloŵe ufumu ndiwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma chifundo changa sichidzamchokera iye, monga ndinachichotsera Saulo amene ndinamchotsa pamaso pako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma sindidzasiya kumukonda, monga ndinachitira ndi Sauli, amene ndinamuchotsa iwe usanakhale mfumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma cifundo canga sicidzamcokera iye, monga ndinacicotsera Sauli amene ndinamcotsa pamaso pako.