2 Samuel 7:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Nanga ine ndingathe kunena chiyaninso kwa Inu? Paja mumandidziŵa mtumiki wanune, Inu Chauta Wamphamvuzonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Davide adzaonjezanso kunenanso ndi Inu? Pakuti mudziwa mnyamata wanu, Yehova Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi Davide anenenso chiyani kwa Inu? Pakuti Inu Ambuye Wamphamvuzonse mukumudziwa mtumiki wanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Davide adzaonjezanso kunenanso ndi Inuj pakuti mudziwa mnyamata wanu, Yehova Mulungu.