2 Samuel 7:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwachita zazikulu zonsezi chifukwa cha lonjezo lanu, ndiponso potsata zimene mtima wanu umafuna, kuti mtumiki wanune ndidziŵe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa cha mau anu, ndi monga mwa mtima wanu, munachita ukulu wonse umene kuuzindikiritsa mnyamata wanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa cha mawu anu komanso mwa chifuniro chanu, mwachita chinthu chachikulu ichi ndipo mwachiwulula kwa mtumiki wanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa ca mau anu, ndi monga mwa mtima wanu, munacita ukuru wonse umene kuuzindikiritsa mnyamata wanu.