2 Samuel 7:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudadzikhazikitsira anthu anu Aisraele kuti akhale anthu anuanu mpaka muyaya. Ndipo Inu Chauta mudakhala Mulungu wao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mwadzikhazikira anthu anu Aisraele, akhale anthu anu nthawi zonse, ndipo Inu Yehova munakhala Mulungu wao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mwawapanga anthu anu Aisraeli kukhala anuanu kwamuyaya, ndipo Inu, Inu Yehova ndinu Mulungu wawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mwadzikhazikira anthu anu Aisrayeli, akhale anthu anu nthawi zonse, ndipo Inu Yehova munakhala Mulungu wao.