2 Samuel 7:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo tsopano Inu Chauta Wamphamvuzonse, ndinu Mulungu, ndipo mau anu ngoona. Mwalonjeza kuti mudzandichitira zabwino zotere ine mtumiki wanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo tsopano, Yehova Mulungu, Inu ndinu Mulungu, ndi mau anu adzakhala oona, ndipo Inu munalonjezana ndi mnyamata wanu kumchitira chabwino ichi,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu Ambuye Wamphamvuzonse, ndinu Mulungu! Mawu anu ndi odalirika, ndipo mwalonjeza zinthu zabwinozi kwa mtumiki wanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo tsopano, Yehova Mulungu, Inu ndinu Mulungu, ndi mau anu adzakhala oona, ndipo Inu munaloniezana ndi mnyamata wanu kumcitira cabwino ici,