2 Samuel 8:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mbiri ya Davide idamveka ponseponse. Pamene ankabwerera, anali atapha Aedomu 18,000 ku chigwa cha Mchere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Davide anamveketsa dzina lake pamene anabwera uko adakantha Aaramu m'Chigwa cha Mchere, ndiwo anthu zikwi khumi mphambu zisanu ndi zitatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Davide anatchuka atabwera kokakantha Aedomu 18,000 mu Chigwa cha Mchere.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Davide anamveketsa dzina lace pamene anabwera uko adakantha Aaramu m'cigwa ca mcere, ndiwo anthu zikwi khumi mphambu zisanu ndi zitatu.