2 Thessalonians 1:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja Mulungu mwa chilungamo chake, adzaŵalanga ndi masautso anthu amene amakusautsani inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
popeza nkolungama kwa Mulungu kubwezera chisautso kwa iwo akuchitira inu chisautso,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu ndi wolungama ndipo adzalanga amene amakusautsaniwo
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
popeza nkolungama kwa Mulungu kubwezera cisautso kwa iwo akucitira inu cisautso,