2 Thessalonians 2:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwa njira iliyonse adzanyenga anthu amene adzaonongedwa chifukwa chokana kukonda choona chimene chikadaŵapulumutsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi m'chinyengo chonse cha chosalungama kwa iwo akuonongeka, popeza chikondi cha choonadi sanachilandira, kuti akapulumutsidwe iwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye adzagwiritsa ntchito mtundu uliwonse wachinyengo kupusitsa amene akuwonongeka. Iwo akuwonongeka chifukwa akukana kukonda choonadi ndi kuti apulumutsidwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi m'cinyengo conse ca cosalungama kwa iwo akuonongeka, popeza cikondi ca coonadi sanacisandira, kuti akapulumutsidwe iwo.