2 Thessalonians 2:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero adzalangidwa onse amene sadakhulupirire choona, koma adakondwerera kusalungama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti aweruzidwe onse amene sanakhulupirira choonadi, komatu anakondwera ndi chosalungama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho adzalangidwa onse amene sanakhulupirire choonadi, koma anakondwera mu zoyipa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti aweruzidwe onse amene sanakhulupirira coonadi, komatu anakondwera ndi cosalungama.