2 Thessalonians 2:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iye pamodzi ndi Yesu Khristu Ambuye athu athuzitse mitima yanu ndi kukupatsani mphamvu za kuchita ndi kulankhula zabwino zilizonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
asangalatse mitima yanu, nakhazikitse inu mu ntchito yonse ndi mau onse abwino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
akulimbikitseni ndi kukupatsani mphamvu yogwirira ntchito ndi kuyankhula zabwino zilizonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
asangalatse mitima yanu, nakhazikitse inu mu nchito yonse ndi mau onse abwino.