2 Thessalonians 2:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi simukukumbukira kuti ndinkakuuzani zimenezi muja ndinali kwanuko?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Simukumbukira kodi, kuti pokhala nanu, ndisanachoke ine, ndinakuuzani izi?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi simukukumbukira kuti pamene ndinali nanu pamodzi ndinkakuwuzani zimenezi?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Simukumbukila kodi, kuti pokhala nanu, ndisanacoke ine, ndinakuuzani izi?