2 Thessalonians 3:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndi dzanja langa ndikulemba mau aŵa: “Moni. Ndine, Paulo.” Mauŵa ndi chizindikiro changa m'kalata iliyonse. Ndimalemba motero.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipereka moni ndi dzanja langa Paulo; ndicho chizindikiro m'kalata aliyense; ndiko kulemba kwanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine Paulo, ndikulemba malonje awa ndi dzanja langa, chimene ndi chizindikiro chodziwika mʼmakalata anga onse. Umo ndi mmene ndimalembera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cilankhulo ndi dzanja langa Paulo; ndico cizindikilo m'kalata ali yense; ndiko kulemba kwanga.