2 Thessalonians 3:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mupempherenso kuti Mulungu atipulumutse kwa anthu ovuta ndi oipa, pakuti si onse ali ndi chikhulupiriro.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kuti tilanditsidwe m'manja a anthu osayenera ndi oipa; pakuti si onse ali nacho chikhulupiriro.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo pempherani kuti tilanditsidwe mʼmanja mwa anthu ovuta ndi oyipa, pakuti si onse amene ali nacho chikhulupiriro.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kuti tilanditsidwe m'manja a anthu osayenerandi oipa; pakuti si onse ali naco cikhulupiriro.