2 Thessalonians 3:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja inu nomwe mukudziŵa zimene muyenera kuchita pofuna kutitsanzira. Ife sitinali aulesi pamene tinali pakati panu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mudziwa nokha m'mene muyenera kutitsanza ifemo; pakuti sitinakhala dwakedwake mwa inu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti inu mukudziwa zimene muyenera kuchita pofuna kutitsatira. Ife sitinali alesi pamene tinali nanu
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mudziwa nokha m'mene muyenera kutitsanza ifemo; pakuti sitinakhala dwacedwace mwa inu;