2 Thessalonians 3:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sitidachitetu zimenezi chifukwa choti tilibe mphamvu zopemphera chithandizo kwa inu, koma tinkafuna kukhala chitsanzo choti muzichitsanzira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
si chifukwa tilibe ulamuliro, komatu kuti tidzipereke tokha tikhale kwa inu chitsanzo chanu, kuti mukatitsanze ife.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sitinachite zimenezi chifukwa choti tinalibe mphamvu zolamula kuti mutithandize koma kuti tikhale chitsanzo choti mutsatire.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
si cifukwa tiribe ulamuliro, komatu kuti tidzipereke tokha tikhale kwa inu citsanzo canu, kuti mukatitsanze ife.