2 Timothy 1:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ukudziŵa kuti onse a ku dziko la Asiya adandisiya. Mwa iwowo wina ndi Figelo, wina ndi Heremogene.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ichi uchidziwa, kuti onse a m'Asiya adabwerera kusiyana nane; a iwo ali Figelo ndi Heremogene.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwe udziwa kuti onse a mʼchigawo cha Asiya anandithawa, kuphatikizapo Fugelo ndi Herimogene omwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ici ucidziwa, kuti onse a m'Asiya adabwerera kusiyana nane; a iwo ali Fugelo ndi Hermogene,