2 Timothy 2:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma nkhani zopanda pake, zosalemekeza Mulungu, uzipewe, pakuti anthu olankhula zotere adzanka nanyozeranyozera Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma pewa nkhani zopanda pake; pakuti adzapitirira kutsata chisapembedzo,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Upewe nkhani zopanda pake, zosalemekeza Mulungu, chifukwa anthu oyankhula zotere amanka napotokerapotokera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma pewa nkhani zopanda pace; pakuti adzapitirira kutsata cisapembedzo,