2 Timothy 2:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo zophunzitsa zao zidzaloŵerera mu anthu ngati kunyeka kwa chilonda. Mwa anthu ameneŵa wina ndi Himeneo, wina ndi Fileto.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo mau ao adzanyeka chilonda; a iwo ali Himeneo ndi Fileto;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chiphunzitso chawo chidzafalikira ngati chilonda. Mwa anthuwa muli Humenayo ndi Fileto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo mau ao adzanyeka cironda; a iwo ali Humenayo ndi Fileto;