2 Timothy 2:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'nyumba yaikulu simukhala ziŵiya zagolide kapena zasiliva zokhazokha; mumakhalanso zamtengo kapena zadothi. Zina zimakhala za ntchito zolemerera, zina za ntchito wamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma m'nyumba yaikulu simuli zotengera za golide ndi siliva zokha, komatunso za mtengo ndi dothi; ndipo zina zaulemu, koma zina zopanda ulemu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼnyumba yayikulu simukhala ziwiya zagolide ndi zasiliva zokha, koma mumakhalanso zamtengo ndi zadothi. Zina zimakhala za ntchito yapamwamba, zina za ntchito wamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma m'nyumba yaikuru simuli zotengera za golidi ndi siliva zokha, komatunso za mtengo ndi dothi; ndipo zina zaulemu, koma zina zopanda ulemu.