2 Timothy 2:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akhale wofatsa polangiza otsutsana naye. Mwina Mulungu angaŵapatse mwai woti atembenuke ndi kuzindikira choona.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
wolangiza iwo akutsutsana mofatsa; ngati kapena Mulungu awapatse iwo chitembenuziro, kukazindikira choonadi,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Otsutsana naye awalangize mofatsa, mwina Mulungu adzawapatsa mwayi woti asinthike ndi kuzindikira choonadi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
1 wolangiza iwo akutsutsana mofatsa; 2 ngati kapena Mulungu awapatse iwo citembenuziro, kukazindikira coonadi,