2 Timothy 2:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Msilikali amene akumenya nkhondo sasamalako ntchito zakumudzi, chifukwa iye amangofuna kukondweretsa mkulu wa ankhondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Msilikali sakodwa nazo ntchito wamba, kuti akakondweretse iye amene adamlemba usilikali.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Palibe msilikali amene ali pa ntchito amagwiranso ntchito za anthu wamba, iye amafuna kukondweretsa bwana wolamulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Msilikari sakodwa nazo nchito wamba, kuti akakondweretse iye amene adamlemba usilikari.