2 Timothy 2:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu wothamanga pa mpikisano wa liŵiro, sangalandire mphotho ngati sathamanga motsata malamulo a mpikisanowo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ngatinso wina ayesana nao m'makani amasewero, samveka korona ngati sanayesana monga adapangana.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chimodzimodzinso, munthu amene ali pa mpikisano waliwiro, salandira mphotho ya wopambana pokhapokha atatsiriza monga mwa malamulo a mpikisanowo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ngatinso wina ayesana nao m'makani a masewero, sambveka korona ngati sanayesana monga adapangana.