2 Timothy 3:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Udziŵe kuti pa masiku otsiriza kudzafika nthaŵi ya zovuta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma zindikira ichi, kuti masiku otsiriza zidzafika nthawi zowawitsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma dziwa izi: Mʼmasiku otsiriza kudzafika nthawi zoopsa kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma zindikira ici, kuti masiku otsiriza zidzafika nthawi zowawitsa.