2 Timothy 3:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
mazunzo anga, ndi masautso anga, monga amene adaandigwera ku Antiokeya, ku Ikonio ndi ku Listara. Ndidaazunzikadi koopsa! Koma Ambuye adandipulumutsa pa zonsezi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
mazunzo, kumva zowawa; zotere zonga anandichitira m'Antiokeya, m'Ikonio, m'Listara, mazunzo otere onga ndawamva; ndipo m'zonsezi Ambuye anandilanditsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mazunzo anga, masautso anga, monga zinandichitikira ku Antiokeya, ku Ikoniya ndi ku Lusitra. Ndinazunzika kwambiri. Koma Ambuye anandipulumutsa pa zonsezi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
mazunzo, kumva zowawa; zotere zonga anandicitira m'Antiokeya, m'Ikoniya, m'Lustro, mazunzo otere onga ndawamva; ndipo m'zonsezi Ambuye anandilanditsa.