2 Timothy 3:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
m'menemo anthu ochimwa ndi onyenga, adzanka naipiraipira, ndipo azidzanyenga ena nkumanyengedwanso iwo omwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma anthu oipa ndi onyenga, adzaipa chiipire, kusokeretsa ndi kusokeretsedwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pomwe anthu oyipa ndi onyenga adzanka nayipirayipira, kunamiza ena, iwo nʼkumanamizidwanso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma anthu oipa ndi onyenga, adzaipa ciipire, kusokeretsa ndi kusokeretsedwa.