2 Timothy 3:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Malembo amathandiza munthu wa Mulungu kukhala wokhoza kwenikweni, ndi wokonzekeratu kuchita ntchito yabwino iliyonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti munthu wa Mulungu akhale woyenera, wokonzeka kuchita ntchito iliyonse yabwino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti munthu wa Mulungu akonzekere bwino lomwe kugwira ntchito iliyonse yabwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti munthu wa Mulungu akhale woyenera, wokonzeka kucita nchito iri yonse yabwino.