2 Timothy 4:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pobwera unditengereko mwinjiro wanga umene ndidasiya kwa Karpo ku Troasi. Unditengerenso mabuku anga, makamaka aja azikopaŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chofunda chija ndinachisiya ku Troasi kwa Karpo, udze nacho pakudza iwe, ndi mabuku, makamaka zikopa zija zolembedwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pobwera, unditengere chofunda pamwamba chimene ndinachisiya kwa Kupro ku Trowa. Unditengerenso mabuku anga, makamaka aja azikopawa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Copfunda cija ndinacisiya ku Trowa kwa Karpo, udze naco pakudza iwe, ndi mabuku, makamaka zikopa zija zolembedwa.