3 John 1:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndinali ndi zambiri zoti ndikuuze, koma sindingakonde kuzilemba m'kalata.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinali nazo zambiri za kukulembera, komatu sindifuna kukulembera ndi kapezi ndi peni;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndili ndi zambiri zoti ndikulembereni, koma sindikufuna kuzilemba mʼkalata.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinali nazo zambiriza kukulembera, komatu sindifuna kukulembera ndi kapezi ndi peni;