3 John 1:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ine ndidaakondwa kwambiri pamene abale ena adafika nkumafotokoza za moyo wako m'choona, ndiponso za m'mene umayendera motsata choona.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ndinakondwera kwakukulu, pofika abale ndi kuchita umboni za choonadi chako, monga umayenda m'choonadi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndinali ndi chimwemwe chachikulu pamene abale ena anafika nʼkundifotokozera za kukhulupirika kwako pa choonadi ndiponso mmene umayendera motsata choonadi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ndinakondwera kwakukuru, pofika abale ndi kucita umboni za coonadi cako, monga umayenda m'coonadi.