3 John 1:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Palibe chondikondweretsa kwambiri koposa kumva kuti ana anga akuyenda m'choona.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndilibe chimwemwe choposa ichi, chakuti ndimva za ana anga kuti alikuyenda m'choonadi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Palibe chondikondweretsa kwambiri kuposa kumva kuti ana anga akukhala mʼchoonadi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiribe cimwemwe coposa ici, cakuti ndimva za ana anga kuti alikuyenda m'coonadi.