3 John 1:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo adachitira umboni chikondi chako pamaso pa mpingo. Ndi bwinodi kuti uŵathandize mokondweretsa Mulungu kupitiriza ulendo wao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
amene anachita umboni za chikondi chako pamaso pa Mpingo; ngati uwaperekeza amenewo pa ulendo wao koyenera Mulungu, udzachita bwino:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anafotokozera mpingo za chikondi chako. Chonde uwathandize kupitiriza ulendo mʼnjira yokondweretsa Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
amene anacita umboni za cikondi cako pamaso pa Mpingo; ngati uwaperekeza amenewo pa ulendo wao koyenera Mulungu, udzacita bwino: