3 John 1:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja adaanyamuka ulendo wao chifukwa cha dzina la Khristu, osalandira thandizo kwa akunja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti chifukwa cha dzinali anatuluka, osalandira kanthu kwa amitundu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti ananyamuka ulendo wawo chifukwa cha dzina la Ambuye, osalandira thandizo kwa osakhulupirira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti cifukwa ca dzinali anaturuka, osalandira kanthu kwa amitundu.